Mbola man

0:00
0:00
Mbola man

Vep tikugwira koma palije chikusintha/ Zinthu kuzikankha koma palije zikusuntha/ pena tikathoka akumat ndife ofuntha/ komano bwanji nde kut tinabadwa ndiminyama/ Nanga bwanji tikasuntha izo zingotimaka/ Guys pena zinthuzi zikutionjeza/ Tilimba mtima bwanji misoz itatilengeza!/ Tikalowa social funs ichuluka zokamba Data off ife timasowa zolengeza!/ Tinena Chan tilibiletu zolengeza/ Tipanga bwanji nanga misoz italengeza/ Ife kukhumbira iwowo akulengeza/ ÷÷÷÷÷÷÷÷÷÷÷÷÷÷÷÷÷ Hayi man mbola mani/ Kusiya vep ndikulakwa mbola man/ Inu pa ufulu Ana anu mbola man/ Koma pena pake man ndimbola man/ "Tsiku lina lakeee/ "chaa pena pake / "Muli ena akee/ "Nthawi ina yake/ " Muli kwina kwake/ "ndaanthu ena ake/ "Inu ndimakape kunena ena ake/ Koma pano munasuntha mwazina lake Nde inu musadandee pali dzina lachee/ chilichose ndichotheka mwazina lache/ Dalisoyu musamude nsiyeni anyadee/

2 Comments

Leave a comment

Author
7 years ago

See track description

3 years ago

WOW ⚡

User avatar
236
Total plays
41
Followers
35
Following

You may also like